2 Mbiri 35:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pambuyo pa zonsezi, Yosiya atakonza nyumba ya Mulungu, Neko+ mfumu ya Iguputo+ anabwera kudzachita nkhondo ku Karikemisi+ pafupi ndi mtsinje wa Firate, ndipo Yosiya+ anapita kukakumana naye.+
20 Pambuyo pa zonsezi, Yosiya atakonza nyumba ya Mulungu, Neko+ mfumu ya Iguputo+ anabwera kudzachita nkhondo ku Karikemisi+ pafupi ndi mtsinje wa Firate, ndipo Yosiya+ anapita kukakumana naye.+