Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 37:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndiyeno anakhala pansi kuti adye chakudya.+ Koma pamene anakweza maso, anaona gulu la apaulendo la Aisimaeli.+ Anali kuchokera ku Giliyadi, ndipo ngamila zawo zinali zitanyamula mafuta onunkhira a labidanamu ndi a basamu, komanso makungwa a utomoni wonunkhira.+ Apaulendowo anali kupita ku Iguputo.

  • Yeremiya 8:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kodi mu Giliyadi+ mulibe mafuta a basamu? Kapena kodi mulibe wochiritsa mmenemo?+ N’chifukwa chiyani nanga mwana wamkazi wa anthu anga sakuchira?+

  • Yeremiya 51:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Babulo wagwa mwadzidzidzi moti wasweka.+ Mulireni mofuula anthu inu.+ M’patseni mafuta a basamu kuti muthetse ululu wake,+ mwina achira.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena