Yesaya 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Akalonga a ku Zowani achita zopusa.+ Akalonga a ku Nofi+ anyengezedwa. Atsogoleri+ a mafuko achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku. Yeremiya 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngakhale anthu a ku Nofi+ ndi ku Tahapanesi+ anawononga dziko lako.*+ Hoseya 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inutu mudzachoka chifukwa dzikolo lidzasakazidwa.+ Anthu a ku Iguputo adzakusonkhanitsani pamodzi+ ndipo anthu a ku Mofi+ adzakuikani m’manda. Zomera zoyabwa zidzamera pakatundu wanu wabwino wasiliva.+ M’mahema mwanu mudzamera zitsamba zaminga.+
13 Akalonga a ku Zowani achita zopusa.+ Akalonga a ku Nofi+ anyengezedwa. Atsogoleri+ a mafuko achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku.
6 Inutu mudzachoka chifukwa dzikolo lidzasakazidwa.+ Anthu a ku Iguputo adzakusonkhanitsani pamodzi+ ndipo anthu a ku Mofi+ adzakuikani m’manda. Zomera zoyabwa zidzamera pakatundu wanu wabwino wasiliva.+ M’mahema mwanu mudzamera zitsamba zaminga.+