1 Mafumu 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumu ya Isiraeli inayankha kuti: “Amuna inu mukamuuze kuti, ‘Musayambe kudzitama nkhondo isanayambe ngati kuti mwapambana kale nkhondoyo.’”+ Miyambo 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dzanja la anthu akhama n’limene lidzalamulire,+ koma dzanja laulesi lidzagwira ntchito yaukapolo.+ Mlaliki 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nthawi ya chikondi ndi nthawi ya chidani ndi munthu.+ Nthawi yankhondo+ ndi nthawi yamtendere.+
11 Mfumu ya Isiraeli inayankha kuti: “Amuna inu mukamuuze kuti, ‘Musayambe kudzitama nkhondo isanayambe ngati kuti mwapambana kale nkhondoyo.’”+
24 Dzanja la anthu akhama n’limene lidzalamulire,+ koma dzanja laulesi lidzagwira ntchito yaukapolo.+