Nahumu 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi iwe uli pabwino kuposa No-amoni+ amene anali pafupi ndi ngalande zochokera mumtsinje wa Nailo?+ Iye anali wozunguliridwa ndi madzi. Chuma chake chinali kuchokera m’nyanja, ndipo nyanjayo ndiyo inali khoma lake.
8 Kodi iwe uli pabwino kuposa No-amoni+ amene anali pafupi ndi ngalande zochokera mumtsinje wa Nailo?+ Iye anali wozunguliridwa ndi madzi. Chuma chake chinali kuchokera m’nyanja, ndipo nyanjayo ndiyo inali khoma lake.