Ezekieli 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzabwezeretsa gulu la Aiguputo amene anagwidwa n’kupita nawo kudziko lina. Ndidzawabwezeretsa kudera la Patirosi,+ m’dziko limene anachokera. Kumeneko adzakhazikitsa ufumu wonyozeka.
14 Ndidzabwezeretsa gulu la Aiguputo amene anagwidwa n’kupita nawo kudziko lina. Ndidzawabwezeretsa kudera la Patirosi,+ m’dziko limene anachokera. Kumeneko adzakhazikitsa ufumu wonyozeka.