Levitiko 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Asamete mpala mitu yawo,+ asamete ndevu za m’masaya mwawo+ ndipo asadzitemeteme thupi lawo.+ Deuteronomo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu.+ Musamadzichekecheke+ kapena kumeta+ nsidze* zanu chifukwa cha anthu akufa. Yeremiya 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Anthu onse a m’dzikoli, osasiyapo aliyense, adzafa ndithu. Sadzaikidwa m’manda+ ndipo anthu sadzadziguguda pachifuwa chifukwa cha iwo. Palibe aliyense amene adzadzichekacheka+ kapena kumeta mpala chifukwa cha iwo.+ Yeremiya 48:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Mutu uliwonse wametedwa mpala,+ ndipo ndevu zonse n’zometa.+ M’manja monse ndi mochekekachekeka,+ ndipo anthu onse amanga ziguduli m’chiuno mwawo.’”+
14 “Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu.+ Musamadzichekecheke+ kapena kumeta+ nsidze* zanu chifukwa cha anthu akufa.
6 ‘Anthu onse a m’dzikoli, osasiyapo aliyense, adzafa ndithu. Sadzaikidwa m’manda+ ndipo anthu sadzadziguguda pachifuwa chifukwa cha iwo. Palibe aliyense amene adzadzichekacheka+ kapena kumeta mpala chifukwa cha iwo.+
37 Mutu uliwonse wametedwa mpala,+ ndipo ndevu zonse n’zometa.+ M’manja monse ndi mochekekachekeka,+ ndipo anthu onse amanga ziguduli m’chiuno mwawo.’”+