Ezekieli 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ine ndidzaonetsa adani awo malo otsetsereka a ku Mowabu. Kumalo amenewa ndi kumene kuli mizinda ya m’malire a dzikolo. Mizinda yake ndi Beti-yesimoti,+ Baala-meoni+ ndi Kiriyataimu.+ Mizinda imeneyi imakongoletsa dzikolo.
9 ine ndidzaonetsa adani awo malo otsetsereka a ku Mowabu. Kumalo amenewa ndi kumene kuli mizinda ya m’malire a dzikolo. Mizinda yake ndi Beti-yesimoti,+ Baala-meoni+ ndi Kiriyataimu.+ Mizinda imeneyi imakongoletsa dzikolo.