Aroma 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Amenewa ngakhale kuti amalidziwa bwino lamulo lolungama la Mulungu,+ lakuti amene amachita zinthu zimenezi n’ngoyenera imfa,+ iwo amapitiriza kuzichita. Kuwonjezera apo, amagwirizananso+ ndi anthu amene amachita zimenezo.
32 Amenewa ngakhale kuti amalidziwa bwino lamulo lolungama la Mulungu,+ lakuti amene amachita zinthu zimenezi n’ngoyenera imfa,+ iwo amapitiriza kuzichita. Kuwonjezera apo, amagwirizananso+ ndi anthu amene amachita zimenezo.