1 Samueli 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Eli anamva phokoso la kulira kwa anthuwo, ndipo anati: “Kodi chisokonezo chikuchitika kumeneku n’chachiyani?”+ Kenako mwamuna uja anathamanga kukauza Eli.
14 Choncho Eli anamva phokoso la kulira kwa anthuwo, ndipo anati: “Kodi chisokonezo chikuchitika kumeneku n’chachiyani?”+ Kenako mwamuna uja anathamanga kukauza Eli.