Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 16:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ife tamva za kunyada kwa Mowabu, kuti ndi wonyada kwambiri.+ Tamva za kudzikweza kwake, kunyada kwake, ndi mkwiyo wake.+ Zolankhula zake zodzitukumula sizidzachitika.+

  • Yesaya 44:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndimalepheretsa zizindikiro za anthu olankhula zinthu zopanda pake, ndipo ndine amene ndimachititsa olosera kuchita zamisala.+ Ndine amene ndimachititsa anthu anzeru kubwerera kumbuyo, ndiponso amene ndimachititsa nzeru zawo kukhala zopusa.+

  • Yeremiya 50:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Lupanga lidzawononga anthu olankhula zinthu zopanda pake.+ Anthu amenewo adzachita zinthu mopanda nzeru.+ Lupanga lidzawononga anthu amphamvu a m’Babulo,+ moti adzagwidwa ndi mantha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena