Salimo 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova wasokoneza zolinga za anthu a mitundu ina.+Walepheretsa maganizo a mitundu ya anthu.+ Miyambo 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Palibe nzeru kapena kuzindikira kulikonse, kapena malangizo alionse otsutsana ndi Yehova.+