Numeri 22:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Kumeneko Balaki anapereka nsembe za nyama ya ng’ombe ndi nkhosa,+ n’kutumiza ina kwa Balamu ndi akalonga amene anali nawo limodzi. Yesaya 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako zinaoneka kuti Mowabu anatopa pamalo okwezeka,+ ndipo anapita kumalo opatulika kukapemphera+ koma sizinathandize.+
40 Kumeneko Balaki anapereka nsembe za nyama ya ng’ombe ndi nkhosa,+ n’kutumiza ina kwa Balamu ndi akalonga amene anali nawo limodzi.
12 Kenako zinaoneka kuti Mowabu anatopa pamalo okwezeka,+ ndipo anapita kumalo opatulika kukapemphera+ koma sizinathandize.+