Salimo 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzavumbitsira oipa misampha, moto ndi sulufule,+Komanso mphepo yotentha, monga gawo limene ayenera kumwa.+ Yesaya 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mantha, dzenje ndi msampha zili pa iwe, munthu wokhala m’dzikoli.+
6 Iye adzavumbitsira oipa misampha, moto ndi sulufule,+Komanso mphepo yotentha, monga gawo limene ayenera kumwa.+