Obadiya 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi pa tsiku limenelo sindidzawononga anthu anzeru mu Edomu?”+ watero Yehova. “Ndiponso kodi sindidzawononga anthu ozindikira a m’dera lamapiri la Esau?
8 Kodi pa tsiku limenelo sindidzawononga anthu anzeru mu Edomu?”+ watero Yehova. “Ndiponso kodi sindidzawononga anthu ozindikira a m’dera lamapiri la Esau?