Yesaya 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Madzulo kudzakhala zoopsa zamwadzidzidzi. Kusanache, zidzachoka.+ Izi n’zimene zidzachitikire anthu otilanda zinthu, ndipo n’zimene zidzagwere anthu oba katundu wathu.+
14 Madzulo kudzakhala zoopsa zamwadzidzidzi. Kusanache, zidzachoka.+ Izi n’zimene zidzachitikire anthu otilanda zinthu, ndipo n’zimene zidzagwere anthu oba katundu wathu.+