Yesaya 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Elamu+ watenga kachikwama koikamo mivi. Iye wakwera galeta lankhondo lonyamula anthu lokokedwa ndi mahatchi, ndipo Kiri+ wasolola chishango. Yeremiya 51:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Wofunkha adzafikira Babulo+ ndipo amuna ake amphamvu adzagwidwa.+ Mauta awo adzathyoledwa,+ pakuti Yehova ndi Mulungu wobwezera.+ Iye adzawabwezera ndithu.+
6 Elamu+ watenga kachikwama koikamo mivi. Iye wakwera galeta lankhondo lonyamula anthu lokokedwa ndi mahatchi, ndipo Kiri+ wasolola chishango.
56 Wofunkha adzafikira Babulo+ ndipo amuna ake amphamvu adzagwidwa.+ Mauta awo adzathyoledwa,+ pakuti Yehova ndi Mulungu wobwezera.+ Iye adzawabwezera ndithu.+