Salimo 69:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atsanulireni matemberero anu,+Ndipo mkwiyo woyaka moto uwagwere.+ Salimo 90:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndani angadziwe kukula kwa ukali wanu,+Ndi kukula kwa mkwiyo wanu kumene kumafanana ndi ulemu umene muyenera kulandira?+
11 Ndani angadziwe kukula kwa ukali wanu,+Ndi kukula kwa mkwiyo wanu kumene kumafanana ndi ulemu umene muyenera kulandira?+