Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 35:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Deralo lidzachitadi maluwa.+ Lidzasangalala ndipo lidzakondwera n’kufuula ndi chisangalalo.+ Lidzapatsidwa ulemerero wa Lebanoni+ ndi kukongola kwa Karimeli+ ndiponso kwa Sharoni.+ Padzakhala anthu amene adzaone ulemerero wa Yehova+ ndi kukongola kwa Mulungu wathu.+

  • Ezekieli 34:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Nkhosazo ndidzazidyetsera m’malo a msipu wabwino ndipo zizidzakhala m’mapiri ataliatali a ku Isiraeli.+ Kumeneko zizidzagona pansi m’malo abwino kwambiri.+ Zizidzadya msipu wobiriwira bwino m’mapiri a ku Isiraeli.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena