Yesaya 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo akuchokera kudziko lakutali.+ Akuchokera kumalekezero a kumwamba. Yehova akubwera ndi zida za mkwiyo wake, kuti asakaze dziko lonse lapansi.+ Yeremiya 51:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Nolani mivi yanu.+ Dzitetezeni ndi zishango zozungulira, amuna inu. Yehova wautsa mitima ya mafumu a Amedi,+ chifukwa akufuna kulanga Babulo ndi kumuwononga.+ Yehova akufuna kubwezera Babulo chilango chifukwa cha kachisi wake.+
5 Iwo akuchokera kudziko lakutali.+ Akuchokera kumalekezero a kumwamba. Yehova akubwera ndi zida za mkwiyo wake, kuti asakaze dziko lonse lapansi.+
11 “Nolani mivi yanu.+ Dzitetezeni ndi zishango zozungulira, amuna inu. Yehova wautsa mitima ya mafumu a Amedi,+ chifukwa akufuna kulanga Babulo ndi kumuwononga.+ Yehova akufuna kubwezera Babulo chilango chifukwa cha kachisi wake.+