Yesaya 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti dzanja la Yehova lidzakhazikika paphiri limeneli,+ ndipo Mowabu adzapondedwapondedwa+ pamalo pake ngati mulu wa udzu umene umapondedwapondedwa pamalo opangira manyowa.+
10 Pakuti dzanja la Yehova lidzakhazikika paphiri limeneli,+ ndipo Mowabu adzapondedwapondedwa+ pamalo pake ngati mulu wa udzu umene umapondedwapondedwa pamalo opangira manyowa.+