Salimo 137:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo, amene udzafunkhidwa,+Wodala ndi amene adzakubwezera+Zimene iwe watichitira.+ Yeremiya 51:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Wofunkha adzafikira Babulo+ ndipo amuna ake amphamvu adzagwidwa.+ Mauta awo adzathyoledwa,+ pakuti Yehova ndi Mulungu wobwezera.+ Iye adzawabwezera ndithu.+
8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo, amene udzafunkhidwa,+Wodala ndi amene adzakubwezera+Zimene iwe watichitira.+
56 Wofunkha adzafikira Babulo+ ndipo amuna ake amphamvu adzagwidwa.+ Mauta awo adzathyoledwa,+ pakuti Yehova ndi Mulungu wobwezera.+ Iye adzawabwezera ndithu.+