Miyambo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kodi kudzikweza kwafika? Ndiye kuti manyazinso afika.+ Koma nzeru zimakhala ndi anthu odzichepetsa.+ Yesaya 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iweyo wanena mumtima mwako kuti, ‘Ndikwera kumwamba.+ Ndikweza mpando wanga wachifumu+ pamwamba pa nyenyezi+ za Mulungu. Ndikhala paphiri lokumanapo+ kumapeto kwenikweni kwa madera a kumpoto.+ Danieli 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mfumuyo inali kunena kuti:+ “Kodi uyu si Babulo Wamkulu amene ine ndamanga ndi mphamvu zanga zazikulu+ ndiponso ndi ulemerero wanga waukulu ndi cholinga chakuti kukhale nyumba yachifumu?”+
2 Kodi kudzikweza kwafika? Ndiye kuti manyazinso afika.+ Koma nzeru zimakhala ndi anthu odzichepetsa.+
13 Iweyo wanena mumtima mwako kuti, ‘Ndikwera kumwamba.+ Ndikweza mpando wanga wachifumu+ pamwamba pa nyenyezi+ za Mulungu. Ndikhala paphiri lokumanapo+ kumapeto kwenikweni kwa madera a kumpoto.+
30 Mfumuyo inali kunena kuti:+ “Kodi uyu si Babulo Wamkulu amene ine ndamanga ndi mphamvu zanga zazikulu+ ndiponso ndi ulemerero wanga waukulu ndi cholinga chakuti kukhale nyumba yachifumu?”+