Yeremiya 51:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Anthu sadzatenga mwala kuchokera kwa iwe kuti ukakhale mwala wapakona kapena mwala wapamaziko+ chifukwa udzakhala mabwinja mpaka kalekale,”+ watero Yehova. Chivumbulutso 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiye chifukwa chake m’tsiku limodzi, miliri yake idzafika. Miliri yakeyo+ ndiyo imfa, kulira, ndi njala. Ndipo adzanyekeratu ndi moto+ chifukwa Yehova Mulungu, amene anamuweruza, ndi wamphamvu.+
26 “Anthu sadzatenga mwala kuchokera kwa iwe kuti ukakhale mwala wapakona kapena mwala wapamaziko+ chifukwa udzakhala mabwinja mpaka kalekale,”+ watero Yehova.
8 Ndiye chifukwa chake m’tsiku limodzi, miliri yake idzafika. Miliri yakeyo+ ndiyo imfa, kulira, ndi njala. Ndipo adzanyekeratu ndi moto+ chifukwa Yehova Mulungu, amene anamuweruza, ndi wamphamvu.+