Zekariya 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamverani! Abusa akulira mofuula+ chifukwa ulemerero wawo watha.+ Tamverani! Mikango yamphamvu ikubangula mofuula chifukwa nkhalango zowirira, za m’mphepete mwa mtsinje wa Yorodano zawonongedwa.+
3 Tamverani! Abusa akulira mofuula+ chifukwa ulemerero wawo watha.+ Tamverani! Mikango yamphamvu ikubangula mofuula chifukwa nkhalango zowirira, za m’mphepete mwa mtsinje wa Yorodano zawonongedwa.+