Yeremiya 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa nthawiyo adzauza anthu awa ndi Yerusalemu kuti: “M’njira zodutsidwadutsidwa za m’chipululu zopita kwa mwana wamkazi wa anthu anga+ mukutuluka mphepo yotentha.+ Mphepo imeneyi si youluzira mankhusu* kapena yoyeretsera tirigu. Yeremiya 49:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anthu a ku Elamu ndidzawabweretsera mphepo zinayi kuchokera kumalekezero anayi a kumwamba.+ Ndidzawabalalitsira kumphepo zonsezi+ ndipo sipadzapezeka mtundu wa anthu kumene obalalitsidwa+ a Elamu sadzapitako.’”
11 Pa nthawiyo adzauza anthu awa ndi Yerusalemu kuti: “M’njira zodutsidwadutsidwa za m’chipululu zopita kwa mwana wamkazi wa anthu anga+ mukutuluka mphepo yotentha.+ Mphepo imeneyi si youluzira mankhusu* kapena yoyeretsera tirigu.
36 Anthu a ku Elamu ndidzawabweretsera mphepo zinayi kuchokera kumalekezero anayi a kumwamba.+ Ndidzawabalalitsira kumphepo zonsezi+ ndipo sipadzapezeka mtundu wa anthu kumene obalalitsidwa+ a Elamu sadzapitako.’”