Yeremiya 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo akamwe ndi kudzandira uku ndi uku ndipo akakhale ngati anthu amisala chifukwa cha lupanga limene ndikuwatumizira pakati pawo.”+ Yeremiya 50:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Madzi ake adzawonongedwa ndipo adzauma.+ Dziko limeneli ndi la zifaniziro zogoba,+ ndipo anthu ake amachita zinthu mosaganiza chifukwa cha masomphenya awo ochititsa mantha.
16 Iwo akamwe ndi kudzandira uku ndi uku ndipo akakhale ngati anthu amisala chifukwa cha lupanga limene ndikuwatumizira pakati pawo.”+
38 Madzi ake adzawonongedwa ndipo adzauma.+ Dziko limeneli ndi la zifaniziro zogoba,+ ndipo anthu ake amachita zinthu mosaganiza chifukwa cha masomphenya awo ochititsa mantha.