Chivumbulutso 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mmodzi wa angelo 7 amene anali ndi mbale 7+ aja, anabwera n’kundiuza kuti: “Bwera, ndikuonetsa chiweruzo cha hule lalikulu+ lokhala pamadzi ambiri,+ Chivumbulutso 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako mngeloyo anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, makamu, mayiko, ndi zinenero.+
17 Mmodzi wa angelo 7 amene anali ndi mbale 7+ aja, anabwera n’kundiuza kuti: “Bwera, ndikuonetsa chiweruzo cha hule lalikulu+ lokhala pamadzi ambiri,+
15 Kenako mngeloyo anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, makamu, mayiko, ndi zinenero.+