Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Habakuku 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “‘Tsoka kwa munthu amene akupezera nyumba yake phindu mwachinyengo.+ Iye akuchita zimenezi kuti amange chisa chake pamalo okwezeka ndi cholinga choti tsoka lisamupeze.+

  • Chivumbulutso 18:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Iwo anathira fumbi pamitu pawo+ akufuula, kulira ndi kumva chisoni,+ ndipo anati, ‘Kalanga ine! Kalanga ine! Mzinda waukuluwu, umene unalemeretsa+ onse okhala ndi ngalawa panyanja+ chifukwa cha chuma chake chamtengo wapatali, pakuti mu ola limodzi, wawonongedwa.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena