Oweruza 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo anali kubwera ndi ziweto zawo ndi mahema awo. Anali kubwera ochuluka kwambiri ngati dzombe,+ ndipo iwo ndi ngamila zawo anali osawerengeka.+ Iwo anali kubwera m’dzikomo n’kumaliwononga.+ Nahumu 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ngakhale utero, moto udzakunyeketsa. Lupanga lidzakuduladula+ ndipo lidzakudya ngati mmene ana a dzombe oyenda pansi amadyera zomera.+ Dzichulukitseni ngati ana a dzombe oyenda pansi, dzichulukitseni ngati dzombe.
5 Iwo anali kubwera ndi ziweto zawo ndi mahema awo. Anali kubwera ochuluka kwambiri ngati dzombe,+ ndipo iwo ndi ngamila zawo anali osawerengeka.+ Iwo anali kubwera m’dzikomo n’kumaliwononga.+
15 Koma ngakhale utero, moto udzakunyeketsa. Lupanga lidzakuduladula+ ndipo lidzakudya ngati mmene ana a dzombe oyenda pansi amadyera zomera.+ Dzichulukitseni ngati ana a dzombe oyenda pansi, dzichulukitseni ngati dzombe.