Yeremiya 50:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Isiraeli ndi nkhosa yosochera.+ Mikango ndi imene yamuchititsa kuthawa.+ Poyamba, mfumu ya Asuri inadya Isiraeli,+ ndipo ulendo uno Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo yakukuta mafupa ake.+ Yeremiya 51:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndidzabwezera Babulo ndi anthu onse okhala m’dziko la Kasidi zoipa zonse zimene anachita ku Ziyoni anthu inu mukuona,”+ watero Yehova.
17 “Isiraeli ndi nkhosa yosochera.+ Mikango ndi imene yamuchititsa kuthawa.+ Poyamba, mfumu ya Asuri inadya Isiraeli,+ ndipo ulendo uno Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo yakukuta mafupa ake.+
24 Ndidzabwezera Babulo ndi anthu onse okhala m’dziko la Kasidi zoipa zonse zimene anachita ku Ziyoni anthu inu mukuona,”+ watero Yehova.