Salimo 44:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwatisandutsa chitonzo kwa anthu oyandikana nafe,+Mwatisandutsa chinthu chonyozeka ndi choseketsa kwa onse otizungulira.+ Salimo 79:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu oyandikana nafe akutitonza,+Anthu otizungulira akutinyoza ndi kutiseka.+
13 Mwatisandutsa chitonzo kwa anthu oyandikana nafe,+Mwatisandutsa chinthu chonyozeka ndi choseketsa kwa onse otizungulira.+