Salimo 79:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 79 Inu Mulungu, anthu a mitundu ina alowa m’dziko limene ndilo cholowa chanu.+Aipitsa kachisi wanu woyera.+Awononga Yerusalemu ndi kumusandutsa bwinja.+ Maliro 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mdani watambasula dzanja lake n’kutenga zinthu+ zake zonse zabwino.Yerusalemu waona mitundu ina itabwera ndi kulowa m’malo ake opatulika,+Mitundu imene munalamula kuti isalowe mumpingo wanu.
79 Inu Mulungu, anthu a mitundu ina alowa m’dziko limene ndilo cholowa chanu.+Aipitsa kachisi wanu woyera.+Awononga Yerusalemu ndi kumusandutsa bwinja.+
10 Mdani watambasula dzanja lake n’kutenga zinthu+ zake zonse zabwino.Yerusalemu waona mitundu ina itabwera ndi kulowa m’malo ake opatulika,+Mitundu imene munalamula kuti isalowe mumpingo wanu.