Ezekieli 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa chifukwa chimenechi, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndikuukira iwe Turo ndipo ndikutumizira mitundu yambiri ya anthu+ kuti idzamenyane nawe. Anthuwo adzabwera ngati mafunde a m’nyanja.+ Chivumbulutso 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako mngeloyo anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, makamu, mayiko, ndi zinenero.+
3 Pa chifukwa chimenechi, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndikuukira iwe Turo ndipo ndikutumizira mitundu yambiri ya anthu+ kuti idzamenyane nawe. Anthuwo adzabwera ngati mafunde a m’nyanja.+
15 Kenako mngeloyo anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, makamu, mayiko, ndi zinenero.+