Deuteronomo 28:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wako lidzakhala ngati mkuwa, ndipo nthaka yako idzakhala ngati chitsulo.+ Salimo 107:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu amene anali opusa chifukwa cha njira yawo yophwanya malamulo,+Komanso chifukwa cha zolakwa zawo, pamapeto pake anadzibweretsera masautso.+ Yeremiya 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho mvula yamvumbi yasiya kugwa,+ ndipo mvula yomalizira siinagwe.+ Ukuchita zinthu mopanda manyazi ngati mkazi amene akuchita uhule.* Palibe chimene chikukuchititsa manyazi.+
23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wako lidzakhala ngati mkuwa, ndipo nthaka yako idzakhala ngati chitsulo.+
17 Anthu amene anali opusa chifukwa cha njira yawo yophwanya malamulo,+Komanso chifukwa cha zolakwa zawo, pamapeto pake anadzibweretsera masautso.+
3 Choncho mvula yamvumbi yasiya kugwa,+ ndipo mvula yomalizira siinagwe.+ Ukuchita zinthu mopanda manyazi ngati mkazi amene akuchita uhule.* Palibe chimene chikukuchititsa manyazi.+