Yeremiya 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yang’anitsitsani zimenezi modabwa, inu kumwamba, ndipo tsitsi lanu liimirire ndi mantha aakulu kwambiri,’ watero Yehova,+ Yeremiya 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mwa aneneri a ku Yerusalemu ndaona zinthu zoopsa.+ Iwo achita chigololo+ ndi kuchita zinthu mwachinyengo.+ Alimbikitsa anthu ochita zoipa kuti aliyense asafooke ndi kusiya+ kuchita zoipa zake. Kwa ine, onsewo akhala ngati Sodomu+ ndipo anthu okhala mumzindawu akhala ngati Gomora.”+ Hoseya 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndaona zinthu zoopsa m’nyumba ya Isiraeli.+ Efuraimu akuchita dama mmenemo.+ Isiraeli wadziipitsa.+
12 Yang’anitsitsani zimenezi modabwa, inu kumwamba, ndipo tsitsi lanu liimirire ndi mantha aakulu kwambiri,’ watero Yehova,+
14 Mwa aneneri a ku Yerusalemu ndaona zinthu zoopsa.+ Iwo achita chigololo+ ndi kuchita zinthu mwachinyengo.+ Alimbikitsa anthu ochita zoipa kuti aliyense asafooke ndi kusiya+ kuchita zoipa zake. Kwa ine, onsewo akhala ngati Sodomu+ ndipo anthu okhala mumzindawu akhala ngati Gomora.”+
10 Ndaona zinthu zoopsa m’nyumba ya Isiraeli.+ Efuraimu akuchita dama mmenemo.+ Isiraeli wadziipitsa.+