Aheberi 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Kalekale, Mulungu analankhula ndi makolo athu nthawi zambiri+ ndiponso m’njira zambiri kudzera mwa aneneri.+
1 Kalekale, Mulungu analankhula ndi makolo athu nthawi zambiri+ ndiponso m’njira zambiri kudzera mwa aneneri.+