Yeremiya 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo ndinanena kuti: “Kalanga ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Kunena zoona, mwapusitsa anthu awa+ ndiponso Yerusalemu mwa kunena kuti, ‘Mudzakhala pa mtendere,’+ koma lupanga lawabaya* mpaka mumtima.” Yeremiya 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno pa tsiku lotsatira, Pasuri anamasula Yeremiya m’matangadzawo.+ Pamenepo Yeremiya anamuuza kuti: “Yehova wanena kuti dzina lako+ silikhalanso Pasuri koma Chochititsa Mantha paliponse.+
10 Pamenepo ndinanena kuti: “Kalanga ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Kunena zoona, mwapusitsa anthu awa+ ndiponso Yerusalemu mwa kunena kuti, ‘Mudzakhala pa mtendere,’+ koma lupanga lawabaya* mpaka mumtima.”
3 Ndiyeno pa tsiku lotsatira, Pasuri anamasula Yeremiya m’matangadzawo.+ Pamenepo Yeremiya anamuuza kuti: “Yehova wanena kuti dzina lako+ silikhalanso Pasuri koma Chochititsa Mantha paliponse.+