Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndipo m’zigawo zonse,+ kulikonse kumene mawu a mfumu ndi lamulo lake zinafika, Ayuda anali ndi chisoni kwambiri+ ndipo anali kusala kudya,+ kubuma ndi kulira mofuula. Ambiri anayala ziguduli+ ndi kuwazapo phulusa+ kuti agonepo.

  • Yeremiya 25:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 “Fuulani, ndipo lirani abusa inu!+ Gubuduzikani pafumbi+ inu anthu otchuka pakati pa gulu la nkhosa,+ chifukwa masiku a kuphedwa ndi kubalalitsidwa kwanu afika+ ndipo mudzagwa ndi kuphwanyika ngati chiwiya chosiririka!+

  • Ezekieli 27:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Iwo adzakulirira mofuula ndi mowawidwa mtima.+ Adzadzithira dothi kumutu+ ndi kugubuduzika paphulusa.+

  • Mika 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Anthu inu musanene zimenezi ku Gati ndipo asakuoneni mukulira.+

      “Gubudukani pafumbi+ m’nyumba ya Afira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena