Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Musatsatire milungu ina, milungu iliyonse ya anthu okuzungulirani,+

  • Deuteronomo 8:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Koma mukadzaiwala Yehova Mulungu wanu, n’kutsatira milungu ina, kuitumikira ndiponso kuigwadira, ndikukuchitirani umboni lero kuti anthu inu mudzatha.+

  • Deuteronomo 11:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 ndipo mudzalandira temberero+ limeneli ngati simudzamvera malamulo a Yehova Mulungu wanu,+ n’kupatuka panjira imene ndikukulamulani lero kuti muziyendamo, n’kuyamba kutsatira milungu ina imene simukuidziwa.

  • Yeremiya 13:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Anthu oipa amenewa akukana kumvera mawu anga.+ Iwo akupitirizabe kuumitsa mitima yawo+ ndipo akutsatira milungu ina kuti aitumikire ndi kuigwadira.+ Anthu amenewa adzakhala ngati lamba ameneyu amene sangagwirenso ntchito iliyonse.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena