Oweruza 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kuwonjezera apo, anatcha mzindawo kuti Dani, kutengera dzina la bambo awo lakuti Dani,+ amene anali wobadwa kwa Isiraeli.+ Ngakhale zili choncho, dzina loyamba la mzindawo linali Laisi.+ 1 Mafumu 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho Beni-hadadi anamvera Mfumu Asa ndipo anatumiza akuluakulu a gulu lake lankhondo kuti akamenyane ndi mizinda ya Isiraeli. Iwo anawononga mizinda ya Iyoni,+ Dani,+ Abele-beti-maaka,+ ndi Kinereti yense mpaka dziko lonse la Nafitali.+
29 Kuwonjezera apo, anatcha mzindawo kuti Dani, kutengera dzina la bambo awo lakuti Dani,+ amene anali wobadwa kwa Isiraeli.+ Ngakhale zili choncho, dzina loyamba la mzindawo linali Laisi.+
20 Choncho Beni-hadadi anamvera Mfumu Asa ndipo anatumiza akuluakulu a gulu lake lankhondo kuti akamenyane ndi mizinda ya Isiraeli. Iwo anawononga mizinda ya Iyoni,+ Dani,+ Abele-beti-maaka,+ ndi Kinereti yense mpaka dziko lonse la Nafitali.+