Salimo 89:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ana ake akadzasiya chilamulo changa,+Ndi kuleka kutsatira zigamulo zanga,+