Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 17:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Dziko limene ukukhalamo ngati mlendoli,+ ndidzalipereka kwa iwe ndi mbewu yako yobwera pambuyo pako. Dziko lonse la Kanani lidzakhala lawo mpaka kalekale, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”+

  • Levitiko 26:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Motero ndidzayendadi pakati panu ndi kukusonyezani kuti ine ndine Mulungu wanu,+ ndipo inu mudzakhala anthu anga.+

  • Ezekieli 11:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 kuti azidzatsatira malamulo anga, azidzasunga zigamulo zanga ndi kuzikwaniritsa.+ Iwo adzakhaladi anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”’+

  • 2 Akorinto 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndipo pali kumvana kotani pakati pa kachisi wa Mulungu ndi mafano?+ Pakuti ifeyo ndife kachisi+ wa Mulungu wamoyo, monga ananenera Mulungu kuti: “Ndidzakhala pakati pawo+ ndi kuyenda pakati pawo. Ndidzakhala Mulungu wawo, ndipo iwo adzakhala anthu anga.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena