Salimo 66:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati ndikuganizira choipa chilichonse mumtima mwanga,Yehova sadzandimvera.+ Hoseya 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwo anapita kukafunafuna Yehova ali ndi nkhosa zawo ndi ng’ombe zawo, koma sanamupeze+ chifukwa anali atawachokera.
6 Iwo anapita kukafunafuna Yehova ali ndi nkhosa zawo ndi ng’ombe zawo, koma sanamupeze+ chifukwa anali atawachokera.