Yakobo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma tsopano mumakonda kudzitama.+ Kunyada konse koteroko ndi koipa.