Salimo 52:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ine ndidzakhala ngati mtengo waukulu wa maolivi+ wa masamba obiriwira m’nyumba ya Mulungu.Ndidzakhulupirira kukoma mtima kosatha kwa Mulungu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Aroma 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngati nthambi zina zinadulidwa, koma iwe ngakhale kuti ndiwe nthambi ya mtengo wa maolivi wam’tchire, unalumikizidwa pakati pa nthambi zotsala+ ndipo unayamba kugawana nawo muzu wamafuta+ wa mtengo wa maoliviwo,+
8 Koma ine ndidzakhala ngati mtengo waukulu wa maolivi+ wa masamba obiriwira m’nyumba ya Mulungu.Ndidzakhulupirira kukoma mtima kosatha kwa Mulungu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+
17 Ngati nthambi zina zinadulidwa, koma iwe ngakhale kuti ndiwe nthambi ya mtengo wa maolivi wam’tchire, unalumikizidwa pakati pa nthambi zotsala+ ndipo unayamba kugawana nawo muzu wamafuta+ wa mtengo wa maoliviwo,+