Salimo 116:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzayenda+ pamaso pa Yehova m’dziko la anthu amoyo.+ Salimo 142:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndinafuula kwa inu kuti mundithandize, inu Yehova.+Ndinanena kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga,+Gawo langa+ m’dziko la amoyo.”+
5 Ndinafuula kwa inu kuti mundithandize, inu Yehova.+Ndinanena kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga,+Gawo langa+ m’dziko la amoyo.”+