Yeremiya 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tamvetserani nkhani imene yamveka! Kugunda kwakukulu kukumveka kuchokera kudziko la kumpoto,+ ndipo kudzasandutsa mizinda ya Yuda kukhala mabwinja, malo obisalamo mimbulu.+ Yeremiya 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yuda akulira maliro+ ndipo zipata zake zagwetsedwa.+ Zagwetsedwa pansi+ ndipo kulira kwa Yerusalemu kwamveka kumwamba.+
22 Tamvetserani nkhani imene yamveka! Kugunda kwakukulu kukumveka kuchokera kudziko la kumpoto,+ ndipo kudzasandutsa mizinda ya Yuda kukhala mabwinja, malo obisalamo mimbulu.+
2 Yuda akulira maliro+ ndipo zipata zake zagwetsedwa.+ Zagwetsedwa pansi+ ndipo kulira kwa Yerusalemu kwamveka kumwamba.+