Yeremiya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Isiraeli anali wopatulika kwa Yehova,+ ndipo anali zipatso zoyambirira kwa Iye.”’+ ‘Anthu onse ofuna kumumeza anali kukhala ndi mlandu+ ndipo tsoka linali kuwagwera,’ watero Yehova.”+ Zekariya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndakwiyira kwambiri anthu a mitundu ina amene akukhala mwabata.+ Ndawakwiyira chifukwa chakuti ine ndinangokwiyira anthu anga pang’ono pokha,+ koma anthu amenewa anakulitsa tsoka la anthu angawo.”’+ Zekariya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo popatsidwa ulemerero,+ Mulungu wandituma kwa anthu a mitundu ina amene anali kukulandani zinthu zanu,+ pakuti Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Amene akukukhudzani,+ akukhudza mwana wa diso langa.+
3 Isiraeli anali wopatulika kwa Yehova,+ ndipo anali zipatso zoyambirira kwa Iye.”’+ ‘Anthu onse ofuna kumumeza anali kukhala ndi mlandu+ ndipo tsoka linali kuwagwera,’ watero Yehova.”+
15 Ndakwiyira kwambiri anthu a mitundu ina amene akukhala mwabata.+ Ndawakwiyira chifukwa chakuti ine ndinangokwiyira anthu anga pang’ono pokha,+ koma anthu amenewa anakulitsa tsoka la anthu angawo.”’+
8 Pambuyo popatsidwa ulemerero,+ Mulungu wandituma kwa anthu a mitundu ina amene anali kukulandani zinthu zanu,+ pakuti Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Amene akukukhudzani,+ akukhudza mwana wa diso langa.+