Miyambo 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu asanagwe, mtima wake umadzikweza,+ ndipo asanapeze ulemerero, amadzichepetsa.+ Yakobo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzichepetseni pamaso pa Yehova,+ ndipo iye adzakukwezani.+